Qur'an ya Chichewa/Chinyanja offline ikupezeka tsopano pa internet.
Ili ndi ndemanga pansi apo ndi apo.
Ndipo theka la Qur'an imeneyi lili mu Chinyanja/ Chichewa chokhachokha, pomwe theka linali lili ndi Arabisch pansi pa Chichewa /Chinyanja.
Izi zachitika Pofuna kuthandiza ma Daiy omwe akupanga Da'wah mma sociale media komanso awo omwe sabva Arabisch.
Ndipo kwa opanga Da'wa pa masamba en mchezo yafewetsedwa motere:
Ndiyotheka kuipanga kopieer en plak kuti pasakhale kulemba chimodzichimodzi. (Gewoon lang klikken om te kopiëren en plakken)
Komanso mutha kumutumizira munthu wina app imeneyi kudzera mkati mwa App yomweyi.